Select Africa Convenient

Convenient

Top Up telephonically from the comfort of your home.
Simple

Simple

No additional paperwork.
Ease-of-Access

Ease of Access

Funds are disbursed within 24 hours.

AS A Civil servant YOU can now conveniently top up your Flexi Loan anytime, anywhere

CIVIL-SERVANT

Malawi USSD FAQs

Do I qualify for a top up?
If you have an existing Flexi Loan with Select, you may qualify for a top-up.
Can the funds be paid into a different account?
No, the funds can only be deposited into the account on record.
Can I change my personal details?
To update your employer, banking, or personal details, please visit your nearest branch or contact our call centre at 088 738 6343/4/5.
Can I change my payment terms?
To adjust your repayment tenure, please visit your nearest branch or contact our call centre at 088 738 6343/4/5.
How soon can I receive the funds?
You can receive the funds within 24 hours. Ts and Cs apply.
Is the USSD service safe?
Yes, Select has a number of checks in place to confirm that your details are correct and are protected at all times. Additionally, Select will keep you informed via SMS throughout the processing of your application. Your funds will be paid into the original bank account on record and cannot be changed during the top-up process, therefore no one can apply on your behalf.
Kodi ndine ololezedwa kutenga ngongole yowonjezera?
Inde ndizotheka ngati muli kale ndi ngongole ndi a Select Financial Services.
Kodi ngongole yanga zingatheke kuti ilowe ku akauti kwina osati yakale ija?
Ayi sizingatheke, ngongole imalowa ku akauti yomwe ilipo kale mu ma buku athu.
Kodi nditha kusintha kalondolondo okhuzana ndi ineyo?
Kuti musinthe kalondolondo wanu wonkhudzana ndi ku ntchito, ku banki, kapena okhudzana ndi inuyo, pitani ku ofesi ya Select imene muli nayo pafupi. Mutha kuyimbaso foni pa 0887386343/4/5 ngati muli kutali ndipo muzathandizidwa moyenerera.
Kodi nditha kusintha nthawi/ zaka zoti ndibwezere ngongole yanga?
Ngati mukufuna kusintha thawi yobwezera ngongole, kapena mulingo odulidwa, pitani ku ofesi yanthu imene muli nayo pafupi kapena ingoyimbani 0887386343/4/5 muzathandizidwa moyenera.
Kodi pamatenga thawi yayitali bwanji kuti ndilandile ndalama?
Ndalama zimatenga maola makumi awiri ndi mphambu zinayi ngati palibe zovuta zilizonse.
Kodi kupanga ndekha ngongole pa lamya nkotetezedwa?
Inde ndinu otetezedwa. A Select alindinjira zingapo zomwe amagwiritsa ntchito, zomwe munthu amayenela kukwanilitsa kuti atenga ngongole. Mongowonjezela, a Select adzakhala akukudziwitsani mmene ndondomeko yanu yosaka ngongole ikuyendela kudzela ku lamya yanu mpaka dongosolori litatha. Ndalama zimalowa ku banki yomwe munalembetsa pathawi yomwe mumatenga ngongole yanu yoyamba, ndipo sizitheka kusintha ndondomeko yanu yaku banki mukamagwiritsa njira imeneyi powonjezera ndalama. Chonchi, palibe angakubeleni.

NEED MORE HELP?

Let one of our consultants help you get the best loan offer.
Call or WhatsApp us on 088 738 6343/4/5

Let us call you. Complete the form in the link below
and one of our Agents will reach out to you shortly